Sheremu akana Khristu, akangana ndi Yakobo, afuna chizindikiro, ndipo akanthidwa ndi Mulungu—Aneneri onse adayankhula za Khristu ndi Chitetezero Chake—Anefi adakhala masiku awo ngati oyendayenda, obadwa m’chisautso, ndi odedwa ndi Alamani. Mdzaka dza pafupifupi 544–421 Yesu asadabadwe.